Ekisodo 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero Mose anafuulira Yehova kuti: “Nditani nawo anthuwa? Angotsala pang’ono kundiponya miyala!”+ Deuteronomo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inuyo ndinu mtolo ndi katundu wolemera. Ndingathe bwanji ndekha kukusenzani, ndi mikangano yanuyo?+
4 Chotero Mose anafuulira Yehova kuti: “Nditani nawo anthuwa? Angotsala pang’ono kundiponya miyala!”+
12 Inuyo ndinu mtolo ndi katundu wolemera. Ndingathe bwanji ndekha kukusenzani, ndi mikangano yanuyo?+