Ekisodo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu mutopa nazo zimenezi, iwe ndi anthu amene uli nawowa, chifukwa ntchito imeneyi yakukulira kwambiri.+ Sungathe kuichita wekha.+ Numeri 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Mose anadandaulira Yehova kuti: “N’chifukwa chiyani mwandivutitsa chonchi ine mtumiki wanu? N’chifukwa chiyani mwandiumira mtima chotere, n’kundisenzetsa chimtolo cha anthu onsewa?+ Numeri 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anthuwo anayamba kukangana+ ndi Mose, kuti: “Zikanakhala bwino tikanangofera limodzi ndi abale athu amene anafa pamaso pa Yehova aja.+ Numeri 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 chifukwa amuna inu munapandukira mawu anga m’chipululu cha Zini, pa nthawi imene khamu lija linakangana nanu.+ Munalephera kundilemekeza+ pa madzi amene anatuluka patsogolo pa khamulo, madzi a Meriba+ ku Kadesi,+ m’chipululu cha Zini.”+
18 Ndithu mutopa nazo zimenezi, iwe ndi anthu amene uli nawowa, chifukwa ntchito imeneyi yakukulira kwambiri.+ Sungathe kuichita wekha.+
11 Ndiyeno Mose anadandaulira Yehova kuti: “N’chifukwa chiyani mwandivutitsa chonchi ine mtumiki wanu? N’chifukwa chiyani mwandiumira mtima chotere, n’kundisenzetsa chimtolo cha anthu onsewa?+
3 Pamenepo anthuwo anayamba kukangana+ ndi Mose, kuti: “Zikanakhala bwino tikanangofera limodzi ndi abale athu amene anafa pamaso pa Yehova aja.+
14 chifukwa amuna inu munapandukira mawu anga m’chipululu cha Zini, pa nthawi imene khamu lija linakangana nanu.+ Munalephera kundilemekeza+ pa madzi amene anatuluka patsogolo pa khamulo, madzi a Meriba+ ku Kadesi,+ m’chipululu cha Zini.”+