Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.”

  • Yesaya 50:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 N’chifukwa chiyani nditabwera sindinapeze aliyense?+ N’chifukwa chiyani nditaitana palibe amene anayankha?+ Kodi dzanja langa lafupika kwambiri moti silingathe kuwombola,+ kapena kodi mwa ine mulibe mphamvu zopulumutsira? Inetu ndimaumitsa nyanja+ pongoidzudzula chabe.+ Mitsinje ndimaisandutsa chipululu.+ Nsomba zake zimanunkha chifukwa chakuti mulibe madzi ndipo zimafa ndi ludzu.+

  • Yesaya 59:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 Dzanja la Yehova silinafupike moti n’kulephera kupulumutsa,+ komanso khutu lake silinagonthe moti n’kulephera kumva.+

  • Maliko 10:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Yesu anawayang’ana ndi kuwauza kuti: “Kwa anthu n’zosathekadi, koma sizili choncho kwa Mulungu, pakuti zinthu zonse n’zotheka ndi Mulungu.”+

  • Luka 1:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Izi zachitika chifukwa zimene Mulungu wanena, sizilephereka.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena