Numeri 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Yehova anamuyankha Mose kuti: “Kodi dzanja la Yehova lafupika lero eti?+ Tsopano uona ngati zimene ndanena zichitikedi kapena ayi.”+ Yesaya 40:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi iwe sukudziwa kapena kodi sunamve?+ Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi, ndiye Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angadziwe zimene iyeyo amazimvetsa.+ Yesaya 59:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Dzanja la Yehova silinafupike moti n’kulephera kupulumutsa,+ komanso khutu lake silinagonthe moti n’kulephera kumva.+
23 Ndiyeno Yehova anamuyankha Mose kuti: “Kodi dzanja la Yehova lafupika lero eti?+ Tsopano uona ngati zimene ndanena zichitikedi kapena ayi.”+
28 Kodi iwe sukudziwa kapena kodi sunamve?+ Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi, ndiye Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angadziwe zimene iyeyo amazimvetsa.+
59 Dzanja la Yehova silinafupike moti n’kulephera kupulumutsa,+ komanso khutu lake silinagonthe moti n’kulephera kumva.+