Numeri 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+ Salimo 78:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iwo analitu kumupandukira kawirikawiri m’chipululu,+Anali kumukhumudwitsa m’chipululumo!+
29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+