Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova atakutumani kuchokera ku Kadesi-barinea+ kuti, ‘Kwerani ndi kukatenga dziko limene ndidzakupatsani kuti likhale lanu,’ pamenepo munapandukiranso malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ ndipo simunasonyeze chikhulupiriro+ mwa iye komanso simunamvere mawu ake.+

  • Salimo 78:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Iwo sanakumbukire dzanja la Mulungu,+

      Sanakumbukire tsiku limene anawawombola kwa mdani wawo,+

  • Salimo 106:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Iwo anayamba kunyansidwa ndi dziko losiririka,+

      Ndipo analibe chikhulupiriro m’mawu ake.+

  • Yohane 12:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Koma ngakhale kuti anachita zizindikiro zambiri pamaso pawo, iwo sanali kukhulupirira iye,

  • Aheberi 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho, tikuona kuti sakanatha kulowa mu mpumulowo chifukwa anali opanda chikhulupiriro.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena