Ekisodo 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Kodi anthu inu mudzakanabe kusunga malamulo ndi malangizo anga kufikira liti?+ Numeri 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+
28 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Kodi anthu inu mudzakanabe kusunga malamulo ndi malangizo anga kufikira liti?+
11 Ndiyeno Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Kodi anthu awa apitiriza kundinyoza kufikira liti?+ Kodi adzayamba liti kundikhulupirira pambuyo pa zizindikiro zonse zimene ndachita pakati pawo?+