Numeri 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 N’chifukwa chiyani Yehova watibweretsa kudziko lino kuti tidzaphedwe ndi lupanga?+ Akazi athu ndi ana athu adzatengedwa ndi adani.+ Kodi si bwino kuti tingobwerera ku Iguputo?”+ Deuteronomo 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ana anu amene munanena kuti: “Adzagwidwa ndi adani!”+ ndiponso ana anu aang’ono amene lero sakudziwa chabwino kapena choipa, amenewa ndiwo adzalowa m’dziko limenelo. Amenewa ndidzawapatsa dzikolo ndipo adzalitenga kukhala lawo.
3 N’chifukwa chiyani Yehova watibweretsa kudziko lino kuti tidzaphedwe ndi lupanga?+ Akazi athu ndi ana athu adzatengedwa ndi adani.+ Kodi si bwino kuti tingobwerera ku Iguputo?”+
39 Koma ana anu amene munanena kuti: “Adzagwidwa ndi adani!”+ ndiponso ana anu aang’ono amene lero sakudziwa chabwino kapena choipa, amenewa ndiwo adzalowa m’dziko limenelo. Amenewa ndidzawapatsa dzikolo ndipo adzalitenga kukhala lawo.