Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Lamulo lililonse ligwire ntchito mofanana kwa mbadwa ndi kwa mlendo wokhala pakati panu.”+

  • Levitiko 22:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Uza Aroni ndi ana ake ndi ana onse a Isiraeli kuti, ‘Mwamuna aliyense wa nyumba ya Isiraeli, kapena mlendo wokhala mu Isiraeli amene akupereka nsembe+ pofuna kukwaniritsa lonjezo lake lililonse,+ kapena amene akupereka nsembe yake yaufulu,+ imene akuipereka kwa Yehova monga nsembe yopsereza,

  • Levitiko 24:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “‘Chigamulo chilichonse chigwire ntchito mofanana pakati panu, kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+

  • Numeri 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Ngati pali mlendo amene akukhala pakati panu, iyenso azikonza nsembe ya pasika yopereka kwa Yehova.+ Aziikonza motsatira malamulo onse a pasika, ndiponso kakonzedwe kake ka nthawi zonse.+ Pakhale malamulo ofanana kwa nonsenu, kaya mlendo kapena mbadwa.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena