Ekisodo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Adzadye nyamayo usiku umenewu.+ Idzakhale yowotcha ndipo adzaidye pamodzi ndi mikate yopanda chofufumitsa+ ndi masamba owawa.+
8 “‘Adzadye nyamayo usiku umenewu.+ Idzakhale yowotcha ndipo adzaidye pamodzi ndi mikate yopanda chofufumitsa+ ndi masamba owawa.+