Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 23:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Mukalowa m’dziko limene ndikukupatsani, n’kukolola mbewu za m’dzikomo, muzibweretsa kwa wansembe mtolo umodzi wa zipatso zanu zoyambirira.+

  • Deuteronomo 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Yehova Mulungu wako akadzakulowetsa m’dziko limene ukupita kukalitenga kukhala lako,+ adzakuchotsera mitundu ikuluikulu.+ Adzakuchotsera Ahiti,+ Agirigasi,+ Aamori,+ Akanani,+ Aperezi,+ Ahivi+ ndi Ayebusi,+ mitundu 7 ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa iwe.+

  • Deuteronomo 26:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Ndiyeno ukakalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa monga cholowa chako, n’kulitenga kukhala lako ndi kukhalamo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena