Salimo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndani angazindikire yekha zinthu zimene walakwitsa?+Mundikhululukire machimo amene ndachita mosadziwa.+ Machitidwe 17:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zoona, Mulungu analekerera nthawi ya kusadziwa koteroko,+ koma tsopano akuuza anthu kwina kulikonse kuti onse alape.+
12 Ndani angazindikire yekha zinthu zimene walakwitsa?+Mundikhululukire machimo amene ndachita mosadziwa.+
30 Zoona, Mulungu analekerera nthawi ya kusadziwa koteroko,+ koma tsopano akuuza anthu kwina kulikonse kuti onse alape.+