Machitidwe 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’mibadwo ya m’mbuyomu iye analola anthu a mitundu yonse kuyenda m’njira zawo.+ Aroma 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mulungu anam’pereka monga nsembe yachiyanjanitso,+ mwa kukhala ndi chikhulupiriro m’magazi ake.+ Mulungu anachita izi pofuna kuonetsa chilungamo chake pokhululuka machimo+ amene anachitika kale, pamene iye anali kusonyeza khalidwe losakwiya msanga,+ Aroma 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Paja Chilamulo chisanabwere, uchimo unalimo kale m’dziko, koma munthu saimbidwa mlandu wa kuchimwa pamene palibe lamulo.+ Aefeso 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene akuyenda motero, alinso mu mdima wa maganizo,+ otalikirana+ ndi moyo wa Mulungu, chifukwa cha umbuli+ umene uli mwa iwo, chifukwanso cha kukakala+ kwa mitima yawo.
25 Mulungu anam’pereka monga nsembe yachiyanjanitso,+ mwa kukhala ndi chikhulupiriro m’magazi ake.+ Mulungu anachita izi pofuna kuonetsa chilungamo chake pokhululuka machimo+ amene anachitika kale, pamene iye anali kusonyeza khalidwe losakwiya msanga,+
13 Paja Chilamulo chisanabwere, uchimo unalimo kale m’dziko, koma munthu saimbidwa mlandu wa kuchimwa pamene palibe lamulo.+
18 Pamene akuyenda motero, alinso mu mdima wa maganizo,+ otalikirana+ ndi moyo wa Mulungu, chifukwa cha umbuli+ umene uli mwa iwo, chifukwanso cha kukakala+ kwa mitima yawo.