Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Ndiyeno zikachitika kuti wina amene wamva mawu a lumbiro+ ili, walankhula modzitama mumtima mwake kuti, ‘Ndidzakhala ndi mtendere+ ngakhale kuti ndidzayenda motsatira zofuna za mtima wanga,’+ koma ali ndi cholinga chowononga wina aliyense, mofanana ndi kukokolola mtengo wothiriridwa bwino ndi wosathiriridwa womwe,

  • Oweruza 17:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Aliyense anali kuchita zimene anali kuona kuti n’zoyenera.+

  • Yobu 31:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ngati ndaponda kumbali kusiya njira,+

      Kapena ngati mtima wanga ukungotsatira maso anga,+

      Kapenanso ngati cholakwa chilichonse chamatirira m’manja mwanga,+

  • Yeremiya 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 koma iwo anapitirizabe kuumitsa mitima yawo+ ndi kutsatira mafano a Baala,+ zinthu zimene anaphunzitsidwa ndi makolo awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena