Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano anthuwo anayamba kudandaula pamaso pa Yehova ngati kuti anali pamavuto.+ Yehova atamva kudandaulako anawapsera mtima, ndipo moto wa Yehova unawayakira n’kupsereza ena a iwo kumalire a msasa.+

  • Numeri 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Kodi khamu la anthu oipa amenewa lidandaula motsutsana nane kufikira liti?+ Ndamva kudandaula konseko kumene ana a Isiraeli akuchita motsutsana nane.+

  • Numeri 16:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zimene mukuchitazi, iweyo limodzi ndi khamu lako lonseli, mukuukira Yehova.+ Kunena za Aroni, kodi iye ndani kuti amuna inu mum’dandaule?”+

  • Numeri 16:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Koma tsiku lotsatira, khamu lonse la ana a Isiraeli linayamba kung’ung’udza motsutsana ndi Mose ndi Aroni,+ kuti: “Mwapha anthu a Yehova inu.”

  • 1 Akorinto 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena