Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 16:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Atafika anauza khamulo kuti: “Chonde, chokani kumahema a anthu oipawa, ndipo musakhudze chinthu chawo chilichonse,+ kuti musaphedwe nawo limodzi chifukwa cha kuchimwa kwawo.”

  • Numeri 16:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Koma tsiku lotsatira, khamu lonse la ana a Isiraeli linayamba kung’ung’udza motsutsana ndi Mose ndi Aroni,+ kuti: “Mwapha anthu a Yehova inu.”

  • Numeri 16:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Amene anaphedwa ndi mliriwo anakwana 14,700, kupatula amene anaphedwa chifukwa cha Kora aja.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena