Numeri 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+ Numeri 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ine ndikutenga Alevi pakati pa ana a Isiraeli m’malo mwa ana onse oyamba kubadwa+ a ana a Isiraeli ndipo iwo akhala anga.
12 “Ine ndikutenga Alevi pakati pa ana a Isiraeli m’malo mwa ana onse oyamba kubadwa+ a ana a Isiraeli ndipo iwo akhala anga.