Levitiko 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nganga ya nsembe yoweyula+ ndiponso mwendo, umene ndi gawo lopatulika, ndikuzitenga pansembe zachiyanjano za ana a Isiraeli. Ndikuzitenga kwa ana a Isiraeli ndi kuzipereka kwa Aroni wansembe ndi ana ake. Ili ndi lamulo mpaka kalekale. Numeri 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Zopereka zonse+ za zinthu zopatulika,+ zimene ana a Isiraeli azipereka kwa wansembe, zizikhala zake.+
34 Nganga ya nsembe yoweyula+ ndiponso mwendo, umene ndi gawo lopatulika, ndikuzitenga pansembe zachiyanjano za ana a Isiraeli. Ndikuzitenga kwa ana a Isiraeli ndi kuzipereka kwa Aroni wansembe ndi ana ake. Ili ndi lamulo mpaka kalekale.
9 “‘Zopereka zonse+ za zinthu zopatulika,+ zimene ana a Isiraeli azipereka kwa wansembe, zizikhala zake.+