Numeri 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zopereka zonse za zinthu zopatulika,+ zimene Aisiraeli azipereka kwa wansembe, zizikhala zake.+