Numeri 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma akazi achimidiyani ndi ana awo anawagwira ndi kuwatenga kupita nawo kwawo.+ Anafunkhanso ziweto zawo zonse ndi chuma chawo chonse. Numeri 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ana aakazi onse aang’ono amene sanagonepo ndi mwamuna musawaphe.+
9 Koma akazi achimidiyani ndi ana awo anawagwira ndi kuwatenga kupita nawo kwawo.+ Anafunkhanso ziweto zawo zonse ndi chuma chawo chonse.