Ekisodo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Usapereke umboni wonamizira mnzako.+ Ekisodo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Usafalitse nkhani yabodza.+ Usagwirizane ndi munthu woipa mwa kukhala mboni yokonzera wina zoipa.+ Miyambo 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Imfa ndiponso moyo zili mu mphamvu ya lilime,+ ndipo wolikonda adzadya zipatso zake.+
23 “Usafalitse nkhani yabodza.+ Usagwirizane ndi munthu woipa mwa kukhala mboni yokonzera wina zoipa.+