Levitiko 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wansembe asakwatire hule+ kapena mkazi amene wataya unamwali wake. Asakwatirenso+ mkazi amene mwamuna wake anamusiya ukwati,+ chifukwa wansembeyo ndi woyera kwa Mulungu wake. Mateyu 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense wothetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha dama,*+ amamuchititsa chigololo akakwatiwanso,+ ndipo aliyense wokwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+ Maliko 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anawauza kuti: “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo+ molakwira mkaziyo.
7 Wansembe asakwatire hule+ kapena mkazi amene wataya unamwali wake. Asakwatirenso+ mkazi amene mwamuna wake anamusiya ukwati,+ chifukwa wansembeyo ndi woyera kwa Mulungu wake.
32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense wothetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha dama,*+ amamuchititsa chigololo akakwatiwanso,+ ndipo aliyense wokwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+
11 Iye anawauza kuti: “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo+ molakwira mkaziyo.