Ezekieli 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo asamatenge mkazi wamasiye kapena wosiyidwa ukwati kuti akhale mkazi wawo,+ koma azitenga anamwali omwe ndi ana ochokera m’nyumba ya Isiraeli+ kapena azitenga mkazi wamasiye amene anali mkazi wa wansembe.’
22 Iwo asamatenge mkazi wamasiye kapena wosiyidwa ukwati kuti akhale mkazi wawo,+ koma azitenga anamwali omwe ndi ana ochokera m’nyumba ya Isiraeli+ kapena azitenga mkazi wamasiye amene anali mkazi wa wansembe.’