Ekisodo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti chofunda chake n’chomwecho.+ Imeneyo ndi nsalu yake yakunja. Adzafunda chiyani pogona? Ndiyeno akandilirira, ine ndidzamumvera ndithu, chifukwa ndine wachifundo.+ Yobu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amathamangitsa ngakhale bulu wamphongo wa ana amasiye,*Amalanda ng’ombe yamphongo ya mkazi wamasiye ngati chikole.+
27 Pakuti chofunda chake n’chomwecho.+ Imeneyo ndi nsalu yake yakunja. Adzafunda chiyani pogona? Ndiyeno akandilirira, ine ndidzamumvera ndithu, chifukwa ndine wachifundo.+
3 Amathamangitsa ngakhale bulu wamphongo wa ana amasiye,*Amalanda ng’ombe yamphongo ya mkazi wamasiye ngati chikole.+