Deuteronomo 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Usapotoze chiweruzo cha mlandu wa mlendo+ kapena mlandu wa mwana wamasiye,*+ ndipo usalande mkazi wamasiye chovala chake monga chikole.+
17 “Usapotoze chiweruzo cha mlandu wa mlendo+ kapena mlandu wa mwana wamasiye,*+ ndipo usalande mkazi wamasiye chovala chake monga chikole.+