Deuteronomo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo mawu awa amene ndikukulamula lero azikhala pamtima pako,+ Salimo 78:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuti anawo azidzadalira Mulungu,+Ndi kuti asadzaiwale zochita za Mulungu+ koma kuti azidzasunga malamulo ake.+ Salimo 119:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti nditsatire chilamulo chanu,+Ndiponso kuti ndichisunge ndi mtima wonse.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
7 Kuti anawo azidzadalira Mulungu,+Ndi kuti asadzaiwale zochita za Mulungu+ koma kuti azidzasunga malamulo ake.+
34 Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti nditsatire chilamulo chanu,+Ndiponso kuti ndichisunge ndi mtima wonse.+
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+