Deuteronomo 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndi kuti adzakukwezani pamwamba pa mitundu ina yonse imene anapanga.+ Zimenezi zidzakudzetserani chitamando, mbiri yabwino ndi kukongola, mukapitiriza kukhala anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu,+ monga mmene anakulonjezerani.”
19 ndi kuti adzakukwezani pamwamba pa mitundu ina yonse imene anapanga.+ Zimenezi zidzakudzetserani chitamando, mbiri yabwino ndi kukongola, mukapitiriza kukhala anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu,+ monga mmene anakulonjezerani.”