Deuteronomo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+ Deuteronomo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+ Salimo 148:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye adzakweza nyanga* ya anthu ake.+Adzachititsa kuti anthu ake onse okhulupirika atamandike,+Amene ndi ana a Isiraeli, anthu amene ali pafupi ndi iye.+Tamandani Ya, anthu inu!+
8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+
28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+
14 Iye adzakweza nyanga* ya anthu ake.+Adzachititsa kuti anthu ake onse okhulupirika atamandike,+Amene ndi ana a Isiraeli, anthu amene ali pafupi ndi iye.+Tamandani Ya, anthu inu!+