Numeri 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musankhe munthu woti akhale mtsogoleri wawo pa zinthu zonse, woti aziwatsogolera pa zochita zawo zonse,+ kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda m’busa.”+ Deuteronomo 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti: “Tsopano ndili ndi zaka 120.+ Sindidzaloledwanso kupitiriza ntchito yanga yokutsogolerani,+ pakuti Yehova wandiuza kuti, ‘Suwoloka Yorodano uyu.’+ 2 Mbiri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mundipatse nzeru ndi luntha lodziwa zinthu+ kuti ndizitha kutsogolera+ anthuwa, pakuti ndani angaweruze anthu anu ochulukawa?”+ Salimo 91:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+Inenso ndidzamupulumutsa.+Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+ Salimo 121:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzakuteteza pa zochita zako zonse,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+
17 Musankhe munthu woti akhale mtsogoleri wawo pa zinthu zonse, woti aziwatsogolera pa zochita zawo zonse,+ kuti khamu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda m’busa.”+
2 kuti: “Tsopano ndili ndi zaka 120.+ Sindidzaloledwanso kupitiriza ntchito yanga yokutsogolerani,+ pakuti Yehova wandiuza kuti, ‘Suwoloka Yorodano uyu.’+
10 Mundipatse nzeru ndi luntha lodziwa zinthu+ kuti ndizitha kutsogolera+ anthuwa, pakuti ndani angaweruze anthu anu ochulukawa?”+
14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+Inenso ndidzamupulumutsa.+Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+