Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Ndidzakwaniritsa pangano langa la pakati pa ine ndi iwe,+ ndi mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe ku mibadwomibadwo. Lidzakhala pangano mpaka kalekale,+ kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbewu yako yobwera pambuyo pa iwe.+

  • Genesis 22:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 n’kumuuza kuti: “Yehova wati, ‘Ndikulumbira+ pali dzina langa, kuti chifukwa cha zimene wachitazi, posakana kupereka mwana wako yekhayo,+

  • Yeremiya 11:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 kuti ndikwaniritse lumbiro limene ndinalumbirira makolo anu+ kuti ndidzawapatsa dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ monga mmene zilili lero.’”’”

      Pamenepo ine ndinayankha kuti: “Zikhale momwemo,* inu Yehova.”

  • Aheberi 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu,+ analumbira pa dzina lake+ chifukwa panalibe wina wamkulu kwa iye amene akanamulumbirira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena