Yesaya 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndiziyembekezera Yehova,+ amene wabisira nkhope yake nyumba ya Yakobo,+ ndipo ndithu ndiziyembekezera iyeyo.+ Yesaya 59:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ayi si choncho. Koma zolakwa za anthu inu n’zimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu,+ ndipo machimo anu amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake, kuti asamve zimene mukunena.+
17 Ine ndiziyembekezera Yehova,+ amene wabisira nkhope yake nyumba ya Yakobo,+ ndipo ndithu ndiziyembekezera iyeyo.+
2 Ayi si choncho. Koma zolakwa za anthu inu n’zimene zakulekanitsani ndi Mulungu wanu,+ ndipo machimo anu amuchititsa kuti akubisireni nkhope yake, kuti asamve zimene mukunena.+