-
Yeremiya 44:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mukudziitanira tsoka mwa kundilakwira ndi ntchito za manja anu. Mukuchita zimenezi mwa kufukiza nsembe zautsi kwa milungu ina+ m’dziko la Iguputo limene munalowamo kuti mukhale monga alendo. Mudziphetsa chifukwa cha zimenezi ndipo mudzakhala otembereredwa ndi otonzedwa pakati pa anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi.+
-