2 Samueli 22:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Alendo adzabwera kwa ine akunthunthumira.+Anthu adzamvetsera mawu anga ndi kuwatsatira.+ Salimo 66:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muuzeni Mulungu kuti: “Ntchito zanu ndi zochititsadi mantha!+Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zanu, adani anu adzabwera kwa inu mogonjera.+ Salimo 81:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma odana kwambiri ndi Yehova adzabwera kwa iye akunjenjemera ndi mantha,+Ndipo nthawi yawo idzakhala mpaka kalekale.
3 Muuzeni Mulungu kuti: “Ntchito zanu ndi zochititsadi mantha!+Chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zanu, adani anu adzabwera kwa inu mogonjera.+
15 Koma odana kwambiri ndi Yehova adzabwera kwa iye akunjenjemera ndi mantha,+Ndipo nthawi yawo idzakhala mpaka kalekale.