Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiwe wodala Isiraeli iwe!+

      Ndani angafanane ndi iwe,+

      Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+

      Chishango chako chokuthandiza,+

      Amenenso ndi lupanga lako lopambana?+

      Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+

      Ndipo iwe udzayendayenda pamalo awo okwezeka.”+

  • 1 Mafumu 10:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Anthu onse a padziko lapansi ankafuna kuonana ndi Solomo, kuti amve nzeru zake zimene Mulungu anaika mumtima mwake.+

  • Yesaya 61:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Alendo adzabwera n’kumaweta ziweto zanu.+ Anthu ochokera kwina+ adzakhala olima minda yanu ndi osamalira minda yanu ya mpesa.+

  • Zekariya 8:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’masiku amenewo, amuna 10 ochokera m’zilankhulo zonse za anthu a mitundu ina+ adzagwira+ chovala cha munthu amene ndi Myuda+ ndi kunena kuti: “Anthu inu tipita nanu limodzi,+ chifukwa tamva kuti Mulungu ali ndi inu.”’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena