Yoswa 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komabe ndikadali ndi mphamvu monga ndinalili pa tsiku limene Mose anandituma.+ Mmene mphamvu zanga zinalili pa nthawiyo, ndi mmenenso zilili panopa, moti ndikhoza kupita kunkhondo ndi kubwerako.+
11 Komabe ndikadali ndi mphamvu monga ndinalili pa tsiku limene Mose anandituma.+ Mmene mphamvu zanga zinalili pa nthawiyo, ndi mmenenso zilili panopa, moti ndikhoza kupita kunkhondo ndi kubwerako.+