Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+

  • Levitiko 26:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “‘Musadzipangire milungu yopanda pake,+ chifaniziro,+ kapena chipilala chopatulika. Musaike mwala wokhala ndi zithunzi zojambula mochita kugoba+ m’dziko lanu kuti muziugwadira,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.

  • Deuteronomo 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Musamale kuti musachite zinthu zokuwonongetsani,+ kutinso musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse, chachimuna kapena chachikazi,+

  • Deuteronomo 4:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Samalani kuti musaiwale pangano la Yehova Mulungu wanu limene anachita nanu,+ ndi kuti musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse chimene Yehova Mulungu wanu anakuletsani.+

  • Deuteronomo 27:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “‘Wotembereredwa ndi munthu aliyense wopanga chifaniziro chosema+ kapena chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula+ ndi kuchibisa. Chifanizirocho ndi chinthu chonyansa kwa Yehova,+ Mulungu wopanga manja a mmisiri wa matabwa ndi zitsulo.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena