Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Bambo anga anali kundilangiza+ kuti: “Mtima wako+ ugwire mwamphamvu mawu anga.+ Sunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo.+

  • Miyambo 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Sunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo+ ndipo usunge lamulo langa ngati mwana+ wako wa diso.

  • Mlaliki 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.

  • Yesaya 48:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje,+ ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a m’nyanja.+

  • 1 Yohane 5:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena