Levitiko 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli, ndiponso mlendo aliyense wokhala mu Isiraeli, wopereka mwana wake aliyense kwa Moleki,*+ aziphedwa ndithu. Nzika za m’dziko lanu zizimupha mwa kum’ponya miyala. Levitiko 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Mwamuna kapena mkazi amene amalankhula ndi mizimu kapena amene amalosera zam’tsogolo+ aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa mwa kuponyedwa miyala. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.’”+ Deuteronomo 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 muzitulutsira mwamuna kapena mkazi wochita chinthu choipayo kunja kwa mzinda, ndipo muzim’ponya miyala kuti afe.+
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli, ndiponso mlendo aliyense wokhala mu Isiraeli, wopereka mwana wake aliyense kwa Moleki,*+ aziphedwa ndithu. Nzika za m’dziko lanu zizimupha mwa kum’ponya miyala.
27 “‘Mwamuna kapena mkazi amene amalankhula ndi mizimu kapena amene amalosera zam’tsogolo+ aziphedwa ndithu.+ Aziphedwa mwa kuponyedwa miyala. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.’”+
5 muzitulutsira mwamuna kapena mkazi wochita chinthu choipayo kunja kwa mzinda, ndipo muzim’ponya miyala kuti afe.+