Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “Dziko limene ndidzakupatsa lidzayambira ku Nyanja Yofiira mpaka kunyanja ya Afilisiti, ndiponso kuyambira kuchipululu mpaka ku Mtsinje.*+ Ndidzachita izi, chifukwa anthu okhala m’dzikomo ndidzawapereka m’manja mwako, ndipo iwe udzawathamangitsa pamaso pako.+

  • Deuteronomo 11:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Malo alionse amene mapazi anu adzapondapo adzakhala anu.+ Malire a dziko lanu adzayambira kuchipululu kukafika ku Lebanoni, kuyambira ku mtsinje wa Firate, kukafika kunyanja ya kumadzulo.+

  • Deuteronomo 12:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno malo amene Yehova Mulungu wako adzasankha kuikapo dzina lake+ akadzakhala kutali kwambiri ndi iwe, uzidzapha zina mwa ng’ombe zako kapena zina mwa nkhosa zako zimene Yehova wakupatsa, monga mmene ndakulamulira, ndipo uzidzadyera mumzinda mwako nyamazo, nthawi iliyonse imene mtima wako wafuna.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena