Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Tsiku limeneli lidzakhala chikumbutso kwa inu, ndipo muzichitira Yehova chikondwerero m’mibadwo yanu yonse. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale, kuti muzichita chikondwerero chimenechi.

  • Ekisodo 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno pa tsiku limenelo udzauze mwana wako kuti, ‘Ndikuchita izi chifukwa cha zimene Yehova anandichitira potuluka mu Iguputo.’+

  • Ekisodo 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chotero mwambo umenewu uzikukumbutsani zimene zinachitikazi ngati chizindikiro cholembedwa padzanja lanu ndi pamphumi panu,+ kuti chilamulo cha Yehova chikhale pakamwa panu.+ Zizikhala choncho chifukwa Yehova anakutulutsani mu Iguputo ndi mphamvu ya dzanja lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena