Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 15:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno Samueli anati: “Kodi sunali kudziona ngati ndiwe mwana+ utakhala mtsogoleri wa mafuko onse a Isiraeli, pamene Yehova anakudzoza+ kuti ukhale mfumu ya Isiraeli?

  • 2 Mbiri 32:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma Hezekiya sanabwezere zabwino zimene anachitiridwa,+ pakuti mtima wake unayamba kudzikuza+ ndipo mkwiyo wa Mulungu+ unayakira iyeyo, Yuda, ndi Yerusalemu.

  • Salimo 131:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 131 Inu Yehova, mtima wanga sunadzikweze,+

      Maso anga si onyada.+

      Sindinafune zinthu zapamwamba kwambiri,+

      Kapena zinthu zodabwitsa kwambiri.+

  • Maliko 10:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Koma Yesu anawaitana, ndipo atafika kwa iye, anawauza kuti: “Inu mukudziwa kuti amene amaoneka ngati akulamulira anthu a mitundu ina amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu awo amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+

  • 1 Petulo 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena