Deuteronomo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukawoloka Yorodano+ ndi kulowa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, muimike miyala ikuluikulu ndi kuipaka utoto woyera. Yoswa 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwalamule kuti, ‘Pitani pakati penipeni pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene ansembe anaimapo chilili,+ mukanyamulepo miyala 12.+ Muisenze ndi kukaiika kumene mugone+ usiku wa lero.’” Yoswa 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthuwo anawoloka mtsinje wa Yorodano pa tsiku la 10 la mwezi woyamba, ndipo anakamanga msasa ku Giligala,+ kumalire a kum’mawa kwa Yeriko.
2 Mukawoloka Yorodano+ ndi kulowa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, muimike miyala ikuluikulu ndi kuipaka utoto woyera.
3 Uwalamule kuti, ‘Pitani pakati penipeni pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene ansembe anaimapo chilili,+ mukanyamulepo miyala 12.+ Muisenze ndi kukaiika kumene mugone+ usiku wa lero.’”
19 Anthuwo anawoloka mtsinje wa Yorodano pa tsiku la 10 la mwezi woyamba, ndipo anakamanga msasa ku Giligala,+ kumalire a kum’mawa kwa Yeriko.