Deuteronomo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukawoloka Yorodano+ ndi kulowa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, muimike miyala ikuluikulu ndi kuipaka utoto woyera. Deuteronomo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yoswa mwana wa Nuni anali wodzazidwa ndi mzimu wa nzeru,+ pakuti Mose anaika manja ake pa iye.+ Choncho ana a Isiraeli anayamba kumumvera ndipo iwo anayamba kuchita monga momwe Yehova analamulira Mose.+
2 Mukawoloka Yorodano+ ndi kulowa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, muimike miyala ikuluikulu ndi kuipaka utoto woyera.
9 Yoswa mwana wa Nuni anali wodzazidwa ndi mzimu wa nzeru,+ pakuti Mose anaika manja ake pa iye.+ Choncho ana a Isiraeli anayamba kumumvera ndipo iwo anayamba kuchita monga momwe Yehova analamulira Mose.+