Yoswa 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano lamula+ ansembe onyamula likasa la pangano. Uwauze kuti: ‘Mukakangofika kumtsinje wa Yorodano, mukalowe m’madzimo ndi kuima+ m’mphepete mwa mtsinjewo.’” Yoswa 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ansembe onyamula likasa la pangano la Yehova anangoima chilili panthaka youma+ pakati pa mtsinje wa Yorodano. Anaimabe choncho pamene Aisiraeli onse anali kuwoloka panthaka youmayo,+ kufikira mtundu wonse unatha kuwoloka mtsinje wa Yorodano.
8 Tsopano lamula+ ansembe onyamula likasa la pangano. Uwauze kuti: ‘Mukakangofika kumtsinje wa Yorodano, mukalowe m’madzimo ndi kuima+ m’mphepete mwa mtsinjewo.’”
17 Ansembe onyamula likasa la pangano la Yehova anangoima chilili panthaka youma+ pakati pa mtsinje wa Yorodano. Anaimabe choncho pamene Aisiraeli onse anali kuwoloka panthaka youmayo,+ kufikira mtundu wonse unatha kuwoloka mtsinje wa Yorodano.