Genesis 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Dziko lonse limene ukulionali, ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako, kuti likhale lanu mpaka kalekale.+ Genesis 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+ Genesis 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ukhale ngati mlendo m’dzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbirira Abulahamu bambo ako.+ Genesis 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakupatsa iwe ndi mbewu zako+ madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti udzakhale mwini dziko limene ukukhalamo ngati mlendo,+ limene Mulungu anapatsa Abulahamu.”+
15 Dziko lonse limene ukulionali, ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako, kuti likhale lanu mpaka kalekale.+
18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+
3 Ukhale ngati mlendo m’dzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbirira Abulahamu bambo ako.+
4 Adzakupatsa iwe ndi mbewu zako+ madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti udzakhale mwini dziko limene ukukhalamo ngati mlendo,+ limene Mulungu anapatsa Abulahamu.”+