-
Yoswa 22:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Chotero tinati, ‘Akadzanena zimenezi kwa ife ndi kwa mibadwo yathu m’tsogolo, ifenso tidzati: “Taonani chifaniziro cha guwa lansembe la Yehova chimene makolo athu anamanga, osati choperekerapo zopereka kapena nsembe zopsereza, koma monga mboni ya pakati pa ife ndi inu.”’
-