Yoswa 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ana ena a Isiraeli anauzidwa+ kuti: “Tamverani! Ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase amanga guwa lansembe m’malire a dziko la Kanani, m’chigawo cha Yorodano kumbali ya ana a Isiraeli.”
11 Kenako ana ena a Isiraeli anauzidwa+ kuti: “Tamverani! Ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase amanga guwa lansembe m’malire a dziko la Kanani, m’chigawo cha Yorodano kumbali ya ana a Isiraeli.”