Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Samalani kuti musadzapereke nsembe zanu zopsereza pamalo ena alionse amene mungaone.+

  • Deuteronomo 12:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ukatero uzipereka nsembe zako zopsereza,+ nyama ndi magazi,+ paguwa lansembe la Yehova Mulungu wako. Magazi a nsembe zako uziwathira pansi pafupi ndi guwa lansembe la Yehova+ Mulungu wako, koma nyamayo utha kuidya.

  • Yoswa 22:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako ana ena a Isiraeli anauzidwa+ kuti: “Tamverani! Ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase amanga guwa lansembe m’malire a dziko la Kanani, m’chigawo cha Yorodano kumbali ya ana a Isiraeli.”

  • 1 Mafumu 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Choncho mfumuyo inakambirana ndi anthu ena+ n’kupanga ana awiri a ng’ombe agolide.+ Itatero inauza anthuwo kuti: “N’zovuta kwambiri kwa inu kuti muzipita ku Yerusalemu. Nayu Mulungu wanu+ Aisiraeli inu, amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena