Miyambo 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nkhawa mumtima mwa munthu ndi imene imauweramitsa,+ koma mawu abwino ndi amene amausangalatsa.+ Miyambo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthumwi yokhulupirika kwa anthu amene aituma ili ngati kuzizira kwa chipale chofewa+ pa tsiku lokolola, chifukwa imatsitsimula moyo wa ambuye ake.+
13 Nthumwi yokhulupirika kwa anthu amene aituma ili ngati kuzizira kwa chipale chofewa+ pa tsiku lokolola, chifukwa imatsitsimula moyo wa ambuye ake.+