Ekisodo 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, likusonyeza kupambana kwa mphamvu zake.+Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, limaphwanya mdani.+ Salimo 89:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mkono wamphamvu ndi wanu,+Dzanja lanu ndi lamphamvu,+Dzanja lanu lamanja ndi lokwezeka.+ Salimo 106:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu anawapulumutsa chifukwa cha dzina lake,+Kuti mphamvu zake zidziwike.+
6 Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, likusonyeza kupambana kwa mphamvu zake.+Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, limaphwanya mdani.+